Surah 110 · 3 verses · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

Surah An-Nasr in Chichewa

In English with tafsir

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

110:1

إِذَا جَآءَ نَصۡرُ ٱللَّهِ وَٱلۡفَتۡحُ

Pamene chithandizo cha Mulungu chidza ndi kupambana

110:2

وَرَأَيۡتَ ٱلنَّاسَ يَدۡخُلُونَ فِي دِينِ ٱللَّهِ أَفۡوَاجًا

Ndipo uona anthu akulowa m’chipembedzo cha Mulungu mu unyinji wawo

110:3

فَسَبِّحۡ بِحَمۡدِ رَبِّكَ وَٱسۡتَغۡفِرۡهُۚ إِنَّهُۥ كَانَ تَوَّابَۢا

Motero lemekeza Ambuye wako ndipo upemphe chikhululukiro chake. Ndithudi Iye amavomera kulapa ndipo ndi wokhululukira

Translation: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.