Surah 1 · 7 verses · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula
Surah Al-Fatihah in Chichewa
1:1
بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ
M’dzina la Mulungu, Mwini Chifundo ndi Mwini Chisoni Chosatha
1:5
إِيَّاكَ نَعۡبُدُ وَإِيَّاكَ نَسۡتَعِينُ
Inu nokha tikulambirani ndipo ndi kwa Inu nokha kumene timapempha chithandizo
1:7
صِرَٰطَ ٱلَّذِينَ أَنۡعَمۡتَ عَلَيۡهِمۡ غَيۡرِ ٱلۡمَغۡضُوبِ عَلَيۡهِمۡ وَلَا ٱلضَّآلِّينَ
Njira ya iwo amene mwawakonda osati ya iwo amene adalandira mkwiyo wanu kapena anasokera
Translation: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.