Surah 108 · 3 verses · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

Surah Al-Kawthar in Chichewa

In English with tafsir

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

108:1

إِنَّآ أَعۡطَيۡنَٰكَ ٱلۡكَوۡثَرَ

Ndithudi takupatsa iwe Mtsinje wa Paradiso

108:2

فَصَلِّ لِرَبِّكَ وَٱنۡحَرۡ

Motero pemphera chifukwa cha Ambuye wako ndipo upereke nsembe

108:3

إِنَّ شَانِئَكَ هُوَ ٱلۡأَبۡتَرُ

Ndithudi aliyense amene akukwiyitsa iwe adzakhala wopanda choyembekezera

Translation: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.