Surah 106 · 4 verses · Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula

Surah Quraysh in Chichewa

In English with tafsir

بِسۡمِ ٱللَّهِ ٱلرَّحۡمَٰنِ ٱلرَّحِيمِ

106:1

لِإِيلَٰفِ قُرَيۡشٍ

Pofuna kuteteza mtundu wa Quraish

106:2

إِۦلَٰفِهِمۡ رِحۡلَةَ ٱلشِّتَآءِ وَٱلصَّيۡفِ

Kuti apitirire pa maulendo nthawi ya Chilimwe ndi m’nthawi ya Chisanu

106:3

فَلۡيَعۡبُدُواْ رَبَّ هَٰذَا ٱلۡبَيۡتِ

Motero auzeni kuti azipembedza Ambuye wa Nyumba ino

106:4

ٱلَّذِيٓ أَطۡعَمَهُم مِّن جُوعٍ وَءَامَنَهُم مِّنۡ خَوۡفِۭ

Amene wawadyetsa m’masiku a njala ndi kuwachotsa mantha

Translation: Al Haji Yusuf Muhammad Kanyamula.